We Believe JesusFé, Esperança e Nova Vida

Yeremiya 9

Biblica® Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero · nianja

← Yeremiya 8 Yeremiya Yeremiya 10 →

1Aa, ndikanakonda kuti mutu wanga ukanakhala chitsime cha madzi,

2Ndani adzandipatsa malo

3“Amapinda lilime lawo ngati uta.

4“Aliyense achenjere ndi abwenzi ake;

5Aliyense amamunamiza mʼbale wake

6Iwe wakhalira mʼchinyengo

7Nʼchifukwa chake Yehova Wamphamvuzonse akuti,

8Lilime lawo lili ngati muvi wakuthwa;

9Kodi ndilekerenji kuwalanga chifukwa cha zimenezi?

10Ndidzakhetsa misozi ndi kulira kwamphamvu chifukwa cha mapiri

11Ndipo Yehova anati, “Ndidzasandutsa Yerusalemu kukhala bwinja,

12Ine ndinati, “Kodi munthu wanzeru ndani woti nʼkumvetsa zimenezi? Kodi ndani amene Yehova anayankhula naye zimenezi kuti akafotokozere ena? Nʼchifukwa chiyani dziko lawonongeka ndi kusanduka chipululu, mʼmene anthu sadutsamo?”

13Yehova anati, “Nʼchifukwa chakuti anthuwa analeka kutsata malamulo anga amene ndinawapatsa; sanandimvere kapena kuwasamala.

14Mʼmalo mwake, anatsatira zolakwa za mʼmitima yawo; anapembedza Abaala ngati momwe makolo awo anawaphunzitsira.”

15Tsono chimene Ine Yehova Wamphamvuzonse, Mulungu wa Israeli ndidzachite ndi anthu amenewa ndi ichi: “Ndidzawadyetsa chakudya cha ziphe ndi kuwamwetsa madzi a ndulu.

16Ndidzawabalalitsa pakati pa mitundu ya anthu imene iwowo kapena makolo awo sanayidziwe, ndipo ndidzawalondola ndi ankhondo mpaka nditawawononga.”

17Yehova Wamphamvuzonse akuti,

18Anthu akuti, “Abwere mofulumira

19Kulira mwachisoni kukumveka kuchokera mu Ziyoni akuti,

20Tsono inu amayi, imvani mawu a Yehova;

21Imfa yatifikira kudzera mʼmazenera athu

22Yehova anandiwuza kuti ndinene izi kuti,

23Yehova akuti,

24koma ngati munthu akufuna kunyadira, anyadire chinthu ichi:

25“Nthawi ikubwera,” akutero Yehova, “pamene ndidzalanga onse amene anachita mdulidwe koma mu mtima sasamala nʼkomwe.

26Ndidzalanga anthu a ku Igupto, Yuda, Edomu, Amoni, Mowabu, ndiponso onse amene amakhala kutali ku chipululu. Mitundu ina yonseyi ndi yosachita mdulidwe, ngakhalenso Aisraeli nawonso sanachite mdulidwe wa mu mtima.”

← Yeremiya 8 Yeremiya Yeremiya 10 →