We Believe JesusFé, Esperança e Nova Vida

Yeremiya 8

Biblica® Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero · nianja

← Yeremiya 7 Yeremiya Yeremiya 9 →

1Yehova akuti, “ ‘Pa nthawi imeneyo, mafupa a mafumu ndi a akuluakulu a ku Yuda, mafupa a ansembe ndi a aneneri, ndiponso mafupa a anthu a ku Yerusalemu adzafukulidwa.

2Adzawamwaza pa nthaka kuyangʼana dzuwa, mwezi ndi nyenyezi zonse zamlengalenga, zimene ankazikonda, kuzitumikira ndi kuzitsatira, kupemphako nzeru ndiponso kuzilambira. Mafupawo sadzawasonkhanitsa kapena kuwakwirira, koma adzakhala ngati ndowe pamwamba pa nthaka.

3Otsala onse a mtundu woyipawu adzafuna imfa kopambana moyo kulikonse kumene ndidzawapirikitsirako, akutero Yehova Wamphamvuzonse.’ ”

4“Tsono awuze anthuwa, ‘Yehova akuti:

5Chifukwa chiyani nanga anthu awa akupitirirabe kuchimwa, osabwerera?

6Ine ndinatchera khutu kumvetsera

7Mbalame yotchedwa kakowa ija imadziwa

8“ ‘Inu mukunena bwanji kuti,

9Anthu anzeru achita manyazi;

10Nʼchifukwa chake akazi awo ndidzawapereka kwa amuna ena

11Iwo amapoletsa zilonda za anthu anga

12Kodi amachita manyazi akamachita zonyansazi?

13“ ‘Ndidzatenga zokolola zawo,

14Koma amati, “Tikukhala pano chifukwa chiyani?

15Tinkayembekezera mtendere

16Kulira kwa ngʼombe zazimuna za mdani

17Yehova akuti, “Onani, ndikukutumizirani njoka zaululu,

18Ndadzazidwa ndi chisoni kwambiri,

19Imvani kulira kwa anthu anga

20“Nthawi yokolola yapita,

21Chifukwa cha mavuto a anthu anga, ine ndikumva kuwawa;

22Kodi ku Giliyadi kulibe mankhwala ochiritsa?

← Yeremiya 7 Yeremiya Yeremiya 9 →