1Inu Aisraeli, imvani zimene Yehova akunena.
2Yehova akuti,
3Pakuti miyambo ya mitundu inayo ndiyachabechabe.
4Amakongoletsa chosemacho ndi siliva ndi golide;
5Mafano awo ali ngati mtengo wakanjedza woopsezera mbalame mʼmunda wa minkhaka.
6Palibe wofanana nanu, Inu Yehova;
7Ndani amene angaleke kukuopani,
8Onsewo ndi opusa ndi opanda nzeru;
9Siliva wosula amabwera naye kuchokera ku Tarisisi
10Koma Yehova ndiye Mulungu woona;
11“Awuze anthu awa kuti, ‘Milungu iyi, imene sinalenge dziko lakumwamba ndi dziko lapansi, idzawonongeka pa dziko lapansi ndi pansi pa thambo.’ ”
12Koma Mulungu analenga dziko lapansi ndi mphamvu zake;
13Iye akayankhula, kumamveka mkokomo wamadzi akumwamba;
14Anthu onse ndi opusa ndiponso opanda nzeru;
15Mafanowo ndi achabechabe, zinthu zosekedwa nazo.
16Koma Yehova amene ndi Cholowa cha Yakobo sali ngati mafanowo.
17Sonkhanitsani katundu wanu,
18Pakuti Yehova akuti,
19Aliyense ankangoti, “Mayo ine, chifukwa cha kupweteka kwanga!
20Tenti yanga yawonongeka,
21Abusa ndi opusa
22Tamvani! kukubwera mphekesera,
23Inu Yehova, ndikudziwa kuti moyo umene munthu ali nawo si wake;
24Inu Yehova, langizeni, komatu mwachilungamo,
25Tsanulirani ukali wanu pa mitundu ya anthu amene sakudziwani,