We Believe JesusFé, Esperança e Nova Vida

Yesaya 30

Biblica® Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero · nianja

← Yesaya 29 Yesaya Yesaya 31 →

1Yehova akuti, “Tsoka kwa ana ondipandukira

2Amapita ku Igupto kukapempha thandizo

3Koma chitetezo cha Farao chidzakhala manyazi anu,

4Ngakhale kuti nduna zawo zili ku Zowani,

5aliyense wa ku Yuda adzachita manyazi

6Uthenga wonena za nyama za ku Negevi:

7Amapita ku Igupto amene thandizo lake ndi lachabechabe.

8Yehova anandiwuza kuti, “Tsopano pita,

9Amenewa ndi anthu owukira, onama ndi

10Iwo amawuza alosi kuti,

11Patukani pa njira ya Yehova,

12Nʼchifukwa chake Woyerayo wa Israeli akunena kuti,

13choncho tchimo linalo lidzakhala ngati mingʼalu

14Lidzaphwanyika ngati mbiya

15Zimene Ambuye Yehova, Woyerayo wa Israeli ananena ndi izi:

16Inu mukuti, ‘Ayi ife tidzathawa,

17Anthu 1,000 mwa inu adzathawa

18Komatu Yehova akufunitsitsa kuti akukomereni mtima,

19Inu anthu a ku Ziyoni, amene mukhala mu Yerusalemu simudzaliranso. Mulungu adzakukomerani mtima pamene adzamva kulira kwanu kopempha thandizo! Ndipo akadzamva, adzakuyankhani.

20Ngakhale Ambuye adzakulowetseni mʼmasautso, aphunzitsi anu sadzakhala kakasi; inu mudzawaona ndi maso anuwo.

21Ngati mudzapatukira kumanja kapena kumanzere, mudzamva mawu kumbuyo kwanu woti, “Njira ndi iyi; yendani mʼmenemo.”

22Pamenepo mudzawononga mafano anu okutidwa ndi siliva ndiponso zifanizo zanu zokutidwa ndi golide; mudzawataya ngati zinthu zonyansa ndipo mudzati, “Zichoke zonsezi!”

23Yehova adzakugwetseraninso mvula pa mbewu zanu zimene mukadzale mʼnthaka, ndipo chakudya chimene mudzakolole chidzakhala chabwino ndi chochuluka. Tsiku limenelo ngʼombe zanu zidzadya msipu wochuluka.

24Ngʼombe ndi abulu amene amalima mʼmunda adzadya chakudya chamchere, chopetedwa ndi foloko ndi fosholo.

25Pa tsiku limene adani anu adzaphedwa ndi nsanja zawo kugwa, mitsinje ya madzi idzayenda pa phiri lililonse lalikulu ndi pa phiri lililonse lalingʼono.

26Mwezi udzawala ngati dzuwa, ndipo kuwala kwa dzuwa kudzawonjezereka kasanu nʼkawiri, ngati kuwala kwa tsiku limodzi. Yehova adzamanga mabala a anthu ake ndi kupoletsa zilonda zimene Iye anachititsa polanga anthu ake.

27Taonani, Yehova akubwera kuchokera kutali,

28Mpweya wake uli ngati mtsinje wosefukira,

29Ndipo inu mudzayimba

30Anthu adzamva liwu la ulemerero la Yehova

31Asiriya adzaopa liwu la Yehova,

32Yehova akamadzalanga adani ake ndi ndodo,

33Malo otenthera zinthu akonzedwa kale;

← Yesaya 29 Yesaya Yesaya 31 →