1Anthu a ku Mowabu
2Monga momwe mbalame zimawulukira uku ndi uku
3Amowabu aja anawuza a ku Yuda kuti,
4Lolani kuti anthu othawa nkhondo a ku Mowabu azikhala pakati panu;
5Mpando waufumu udzakhazikitsidwa mwachikondi;
6Tinamva kuti Mowabu anadzikuza kwambiri.
7Nʼchifukwa chake Amowabu akulira kwambiri;
8Minda ya ku Hesiboni yauma,
9Kotero Ine ndikulira, monga mmene akulirira anthu a ku Yazeri,
10Chimwemwe ndi chisangalalo zalekeka ku minda yanu ya zipatso;
11Chifukwa chake moyo wanga ukulira ngati pangwe kulirira Mowabu,
12Ngakhale anthu a ku Mowabu
13Awa ndi mawu amene Yehova wayankhula kale zokhudza Mowabu.
14Koma tsopano Yehova akuti, “Zisanathe zaka zitatu, potsata mʼmene munthu waganyu amawerengera, ulemerero wa Mowabu udzakhala utatheratu ndipo anthu ake ambiri adzakhala atawonongeka, ndipo opulumuka ake adzakhala ochepa ndi ofowoka.”