1Ana a Israeli anali awa:
2Dani, Yosefe, Benjamini, Nafutali, Gadi ndi Aseri.
3Ana a Yuda anali awa:
4Mpongozi wake Tamara anamuberekera Perezi ndi Zera. Ana onse a Yuda analipo asanu.
5Ana a Perezi anali awa:
6Ana a Zera anali awa:
7Mwana wa Karimi anali
8Mwana wa Etani anali
9Ana amene anabadwa kwa Hezironi anali:
10Ramu anabereka
11Naasoni anabereka Salima, Salima anabereka Bowazi,
12Bowazi anabereka Obedi ndipo Obedi anabereka Yese.
13Yese anabereka
14wachinayi Netaneli, wachisanu Radai,
15wachisanu ndi chimodzi Ozemu ndi wachisanu ndi chiwiri Davide.
16Alongo awo anali Zeruya ndi Abigayeli. Ana atatu a Zeruya anali Abisai Yowabu ndi Asaheli.
17Abigayeli anali amayi ake a Amasa amene abambo ake anali Yeteri wa fuko la Ismaeli.
18Kalebe mwana wa Hezironi anabereka ana mwa Azuba mkazi wake (ndi mwa Yerioti). Ana a mkaziyo anali awa: Yeseri, Sobabu ndi Aridoni.
19Azuba atamwalira, Kalebe anakwatira Efurata, amene anamuberekera Huri.
20Huri anabereka Uri ndipo Uri anabereka Bezaleli.
21Patapita nthawi, Hezironi anagona ndi mwana wamkazi wa Makiri abambo ake a Giliyadi (iye anamukwatira ali ndi zaka 60) ndipo anamuberekera Segubu.
22Segubu anabereka Yairi, amene anali ndi mizinda 23 ku Giliyadi.
23(Koma Gesuri ndi Aramu analanda Havoti Yairi komanso Kenati ndi madera ake onse ozungulira, mizinda makumi asanu ndi umodzi). Onsewa anali adzukulu, a Makiri abambo ake a Giliyadi.
24Atamwalira Hezironi ku Kalebe Efurata, Abiya mkazi wa Hezironi anamuberekera Asihuri abambo a Tekowa.
25Ana a Yerahimeeli, mwana woyamba wa Hezironi anali:
26Yerahimeeli anali ndi mkazi wina amene dzina lake linali Atara, amene anali amayi a Onamu.
27Ana a Ramu, mwana woyamba wa Yerahimeeli, anali awa:
28Ana a Onamu anali awa:
29Mkazi wa Abisuri anali Abihaili, amene anamuberekera Ahibani ndi Molidi.
30Ana a Nadabu anali awa:
31Ana a Apaimu anali awa:
32Ana a Yada, mʼbale wa Samai, anali awa:
33Ana a Yonatani anali awa:
34Sesani sanabereke ana aamuna koma aakazi okhaokha.
35Sesani anapereka mwana wake wamkazi kwa Yariha wantchito wake kuti amukwatire ndipo anamuberekera Atayi.
36Atayi anali abambo ake a Natani,
37Zabadi anali abambo a Efilali,
38Obedi anali abambo a Yehu,
39Azariya anali abambo a Helezi,
40Eleasa anali abambo ake a Sisimai,
41Salumu anali abambo a Yekamiya,
42Ana a Kalebe mʼbale wa Yerahimeeli anali awa:
43Ana a Hebroni anali awa:
44Sema anali abambo ake Rahamu ndipo Rahamu anali abambo a Yorikeamu. Rekemu anali abambo a Samai.
45Mwana wa Samai anali Maoni, ndipo Maoni anali abambo a Beti Zuri.
46Efai, mzikazi wa Kalebe, anali amayi a Harani, Moza ndi Gazezi. Harani anali abambo a Gazezi.
47Ana a Yahidai anali awa:
48Maaka mzikazi wa Kalebe anali mayi Seberi ndi Tirihana.
49Iye anaberekanso Saafi abambo a Madimena ndi Seva abambo a Makibena ndi Gibeya. Mwana wamkazi wa Kalebe anali Akisa.
50Izi zinali zidzukulu za Kalebe.
51Salima abambo a Betelehemu ndi Harefu abambo ake a Beti-Gadera.
52Zidzukulu za Sobala abambo a Kiriati Yearimu zinali izi:
53ndipo mabanja a Kiriati-Yeyarimu anali awa: Aitiri, Aputi, Asumati ndi Amisirai. Azorati ndi Aesitaoli anachokera kwa amenewa.
54Zidzukulu za Salima zinali izi:
55ndiponso mabanja a alembi amene amakhala ku Yabesi: Atiroti, Asimeati ndiponso Asukati. Awa ndi Akeni amene anachokera kwa Hamati, kholo la Arekabu.