1Ana aamuna a Davide amene anabadwira ku Hebroni anali awa:
2wachitatu anali Abisalomu, mwana wa Maaka mwana wa Talimai mfumu ya Gesuri;
3wachisanu anali Sefatiya, amayi ake anali Abitali;
4Ana asanu ndi mmodzi awa a Davide anabadwira ku Hebroni kumene analamulirako zaka zisanu ndi ziwiri ndi miyezi isanu ndi umodzi.
5ndipo ana amene anabadwira ku Yerusalemuko anali awa:
6Anaberekanso Ibihari, Elisua, Elipeleti,
7Noga, Nefegi, Yafiya,
8Elisama, Eliada ndi Elifeleti, onse analipo asanu ndi anayi.
9Onsewa anali ana a Davide, osawerengera ana a azikazi. Ndipo mlongo wawo anali Tamara.
10Mwana wa Solomoni anali Rehabiamu,
11Yehosafati anabereka Yehoramu,
12Yowasi anabereka Amaziya,
13Yotamu anabereka Ahazi,
14Manase anabereka Amoni,
15Ana a Yosiya anali awa:
16Ana a Yehoyakimu:
17Zidzukulu za Yekoniya wa mʼndende zinali izi:
18Malikiramu, Pedaya, Senazara, Yekamiya, Hosama ndi Nedabiya.
19Ana a Pedaya anali awa:
20Panalinso ana ena asanu awa:
21Zidzukulu za Hananiya zinali izi:
22Zidzukulu za Sekaniya zinali izi:
23Ana a Neariya anali awa:
24Ana a Eliyoenai: Hodaviya, Eliyasibu, Pelaya, Akubu,