We Believe JesusFé, Esperança e Nova Vida

1 Mbiri 1

Biblica® Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero · nianja

1 Mbiri 1 Mbiri 2 →

1Adamu, Seti, Enosi

2Kenani, Mahalaleli, Yaredi,

3Enoki, Metusela, Lameki, Nowa.

4Ana a Nowa,

5Ana aamuna a Yafeti anali:

6Ana aamuna a Gomeri anali:

7Ana aamuna a Yavani anali:

8Ana aamuna a Hamu anali:

9Ana aamuna a Kusi anali:

10Kusi anali abambo a Nimurodi amene anali wankhondo wamphamvu

11Igupto ndiye kholo la

12Apaturusi, Akasilu (kumene kunachokera Afilisti) ndi Akafitori.

13Kanaani anabereka mwana wake wachisamba Sidoni,

14Ayebusi, Aamori, Agirigasi

15Ahivi, Aariki, Asini

16Aaravadi, Azemari ndi Ahamati.

17Ana aamuna a Semu anali:

18Aripakisadi anabereka Sela

19Eberi anabereka ana aamuna awiri:

20Yokitani anabereka

21Hadoramu, Uzali, Dikila

22Obali, Abimaeli, Seba,

23Ofiri, Havila ndi Yobabu. Onsewa anali ana aamuna a Yokitani.

24Semu, Aripakisadi, Sela

25Eberi, Pelegi, Reu

26Serugi, Nahori, Tera

27ndi Abramu (amene ndi Abrahamu).

28Ana a Abrahamu ndi awa:

29Zidzukulu zake zinali izi:

30Misima, Duma, Masa, Hadadi, Tema,

31Yeturi, Nafisi ndi Kedema. Awa anali ana a Ismaeli.

32Ana a Ketura mzikazi wa Abrahamu anali awa:

33Ana aamuna a Midiyani anali,

34Abrahamu anabereka Isake.

35Ana aamuna a Esau anali awa:

36Ana a Elifazi anali awa:

37Ana a Reueli anali awa:

38Ana a Seiri anali awa:

39Ana aamuna a Lotani anali awa:

40Ana aamuna a Sobala anali awa:

41Mwana wa Ana anali

42Ana aamuna a Ezeri anali awa:

43Awa ndi mafumu amene ankalamulira dziko la Edomu, mfumu iliyonse ya Israeli isanayambe kulamulira kumeneko:

44Bela atamwalira, Yobabu mwana wa Zera wochokera ku Bozira analowa ufumu mʼmalo mwake.

45Yobabu atamwalira, Husamu wochokera ku dziko la Atemani, analowa ufumu mʼmalo mwake.

46Husamu atamwalira, Hadadi mwana wa Bedadi, amene anagonjetsa Amidiyani mʼdziko la Mowabu, analowa ufumu mʼmalo mwake. Mzinda wake unkatchedwa Aviti.

47Hadadi atamwalira, Samila wochokera ku Masireka analowa ufumu mʼmalo mwake.

48Samila atamwalira, Sauli wochokera ku Rehoboti wa ku Mtsinje analowa ufumu mʼmalo mwake.

49Sauli atamwalira, Baala-Hanani mwana wa Akibori analowa ufumu mʼmalo mwake.

50Pamene Baala-Hanani anamwalira, Hadadi analowa ufumu mʼmalo mwake. Mzinda wake unkatchedwa Pau, ndipo dzina la mkazi wake linali Mehatabeli mwana wa Matiredi, mwana wamkazi wa Me-Zahabu.

51Hadadi anamwaliranso.

52Oholibama, Ela, Pinoni,

53Kenazi, Temani, Mibezari,

54Magidieli ndi Iramu. Awa anali mafumu a ku Edomu.

1 Mbiri 1 Mbiri 2 →