We Believe JesusFé, Esperança e Nova Vida

Yeremiya 51

Biblica® Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero · nianja

← Yeremiya 50 Yeremiya Yeremiya 52 →

1Yehova akuti,

2Ndidzatuma alendo ku Babuloni

3Okoka uta musawalekerere

4Adzavulazidwa ndi kufera mʼdziko la Babuloni

5Pakuti Yuda ndi Israeli sanasiyidwe ngati amasiye

6“Thawaniko ku Babuloni!

7Babuloni anali ngati chikho cha golide mʼdzanja la Yehova;

8Babuloni wagwa mwadzidzidzi ndi kusweka.

9Ena anati, “ ‘Ife tinayesa kumupatsa mankhwala Babuloni,

10“ ‘Yehova waonetsa poyera kuti ndife osalakwa;

11“Yehova wadzutsa mitima ya mafumu a Amedi,

12Kwezani mbendera yankhondo kuti muwononge malinga a Babuloni!

13Inu muli ndi mitsinje yambiri

14Yehova Wamphamvuzonse analumbira pali Iye mwini kuti:

15“Yehova analenga dziko lapansi ndi mphamvu zake;

16Iye akayankhula, kumamveka mkokomo wamadzi akumwamba.

17“Anthu onse ndi opusa ndiponso opanda nzeru;

18Mafanowo ndi achabechabe, zinthu zosekedwa nazo.

19Koma Yehova amene ndi Cholowa cha Yakobo sali ngati mafanowo.

20“Iwe Babuloni ndi ndodo yanga,

21ndi iwe ndimaphwanya kavalo ndi wokwerapo,

22Ndi iwe ndimaphwanya mwamuna ndi mkazi,

23Ndi iwe ndimaphwanya mʼbusa ndi ziweto,

24“Inu mukuona ndidzalanga Babuloni ndi onse amene amakhala mʼdziko la Babuloni chifukwa cha zolakwa zonse anachita ku Ziyoni,” akutero Yehova.

25“Taonani, ndikukuzenga mlandu, iwe phiri lowononga,

26Palibe ngakhale ndi mwala wako umodzi umene anthu adzawutenga

27“Kwezani mbendera ya nkhondo mʼdziko!

28Konzekeretsani mitundu ya anthu.

29Dziko likunjenjemera ndi kunthunthumira,

30Ankhondo a ku Babuloni aleka kuchita nkhondo;

31Othamanga akungopezanapezana,

32Madooko onse alandidwa,

33Yehova Wamphamvuzonse, Mulungu wa Israeli akuti,

34A ku Yerusalemu akuti, “Nebukadinezara mfumu ya ku Babuloni watiwononga,

35Anthu a ku Ziyoni anene kuti,

36Nʼchifukwa chake Yehova akuti,

37Motero Babuloni adzasanduka mulu wa nyumba zogumuka,

38Anthu ake onse adzabangula ngati mkango,

39Ngati achita dyera

40“Ine ndidzawatenga

41“Ndithu Babuloni walandidwa,

42Nyanja yakwera ndi kumiza Babuloni;

43Mizinda yake yasanduka bwinja,

44Ndidzalanga Beli mulungu wa Ababuloni,

45“Tulukani mʼBabuloni anthu anga!

46Musataye mtima kapena kuchita mantha

47Pakuti taonani, nthawi ikubwera ndithu

48Pamenepo kumwamba ndi dziko lapansi ndi zonse zili mʼmenemo

49“Babuloni anapha anthu ambiri pa dziko lapansi.

50Inu amene munapulumuka ku nkhondo ya Babuloni,

51Inu mukuti, “Tikuchita manyazi,

52Nʼchifukwa chake Yehova akuti,

53Ngakhale Babuloni atadzikweza mpaka mlengalenga

54“Imvani mfuwu wolira kuchokera ku Babuloni.

55Pakuti Yehova akuwononga Babuloni,

56Pakuti wowononga wafika kudzamenyana ndi Babuloni,

57Ndidzaledzeretsa akuluakulu ake pamodzi ndi anzeru ake,

58Yehova Wamphamvuzonse akuti,

59Zedekiya mfumu ya Yuda inali ndi phungu wake wamkulu amene dzina lake linali Seraya mwana wa Neriya chidzukulu cha Maseya. Mʼchaka chachinayi cha ulamuliro wake, Zedekiya anapita ndi Seraya ku Babuloni. Tsono mneneri Yeremiya anamupatsirako uthenga Serayayo.

60Yeremiya anali atalemba mʼbuku za masautso onse amene adzafike pa Babuloni ndi zina zonse zokhudza Babuloni.

61Yeremiya anawuza Seraya kuti, “Ukakafika ku Babuloni, ukaonetsetse kuti wawawerengera anthu onse mawu onsewa.

62Ndipo ukanene kuti, ‘Inu Yehova, mwanena kuti mudzawononga malo ano, kotero kuti simudzatsala munthu kapena nyama mʼdziko muno; lidzakhala chipululu mpaka muyaya.’

63Ukakatha kuwerenga bukuli, ukalimangirire ku mwala ndipo ukaliponye pakati pa mtsinje wa Yufurate.

64Ndipo ukanene kuti, ‘Umu ndi mmene adzamirire Babuloni ndipo sadzadzukanso chifukwa cha masautso amene adzamugwere.’ ”

← Yeremiya 50 Yeremiya Yeremiya 52 →