We Believe JesusFé, Esperança e Nova Vida

Yeremiya 46

Biblica® Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero · nianja

← Yeremiya 45 Yeremiya Yeremiya 47 →

1Yehova anamupatsa Yeremiya uthenga wonena za anthu a mitundu ina.

2Kunena za Igupto:

3anati, “Konzani zishango zanu ndi malihawo,

4Mangani akavalo,

5Yeremiya anati: Kodi ndikuona chiyani?

6Waliwiro sangathe kuthawa

7“Kodi ndani amene akukwera ngati Nailo,

8Igupto akusefukira ngati Nailo,

9Tiyeni, inu akavalo!

10Koma tsikulo ndi la Ambuye Yehova Wamphamvuzonse;

11“Pita ku Giliyadi ukatenge mankhwala

12Anthu a mitundu ina amva za manyazi ako;

13Uthenga umene Yehova anapatsa mneneri Yeremiya wonena za kubwera kwa Nebukadinezara mfumu ya ku Babuloni kudzathira nkhondo Igupto ndi uwu:

14“Mulengeze ku Igupto. Mulengeze ku Migidoli.

15Chifukwa chiyani mulungu wanu wamphamvu uja Apisi wathawa?

16Ankhondo anu apunthwa ndi kugwa.

17Kumeneku iwo adzafuwula kuti,

18“Pali Ine wamoyo,” ikutero Mfumu,

19Konzani katundu wanu wopita naye ku ukapolo

20“Igupto ali ngati mwana wangʼombe wokongola,

21Ngakhale ankhondo aganyu amene ali naye

22Aigupto akuthawa ndi liwu lawo lili ngati la njoka yothawa

23Iwo adzadula nkhalango ya Igupto,”

24Anthu a ku Igupto achita manyazi

25Yehova Wamphamvuzonse, Mulungu wa Israeli, akunena kuti, “Ndili pafupi kulanga Amoni mulungu wa Tebesi. Ndidzalanganso Farao ndi Igupto pamodzi ndi milungu yake yonse, mafumu ake ndi onse amene amamukhulupirira.

26Ndidzawapereka kwa amene akufuna kuwapha, ndiye kuti kwa Nebukadinezara mfumu ya ku Babuloni ndi atsogoleri ake ankhondo. Komabe, mʼtsogolomo Igupto adzakhalanso ndi anthu monga kale,” akutero Yehova.

27“Iwe mtumiki wanga Yakobo, usachite mantha;

28Iwe mtumiki wanga Yakobo, usachite mantha,

← Yeremiya 45 Yeremiya Yeremiya 47 →