1Yehova anawuza Yeremiya kuti,
2“Ine Yehova, Mulungu wa Israeli ndikuti, ‘Lemba mʼbuku mawu onse amene ndakuwuza.
3Nthawi ikubwera pamene ndidzachotse anthu anga, Israeli ndi Yuda kuchokera ku ukapolo ndi kuwabwezera dziko limene ndinapatsa makolo awo,’ akutero Yehova.”
4Nawa mawu amene Yehova anayankhula ndi anthu a ku Israeli ndi Yuda:
5“Yehova akuti:
6Tsono khalani pansi ndi kudzifunsa kuti:
7Mayo ine! Tsiku limeneli ndi lalikulu kwambiri!
8Yehova Wamphamvuzonse akuti, “Pa tsiku limenelo,
9Mʼmalo mwake, adzatumikira Yehova Mulungu wawo
10“ ‘Tsono usachite mantha, iwe mtumiki wanga Yakobo;
11Ine ndili nanu ndipo ndidzakupulumutsani,’
12Yehova akuti,
13Palibe amene angathe kukutetezani pa mlandu wanu,
14Abwenzi anu onse akuyiwalani;
15Chifukwa chiyani mukulira nacho chilonda chanu?
16“Tsono onse amene anakuwonongani, nawonso adzawonongedwa;
17Ndidzachiza matenda anu
18Yehova akuti,
19Anthuwo adzayimba nyimbo zoyamika Yehova
20Ana awo adzakhalanso monga mmene analili kale,
21Mtsogoleri wawo adzakhala mmodzi mwa iwo.
22“Choncho inu mudzakhala anthu anga,
23Taonani ukali wa Yehova wowomba
24Mkwiyo woopsa wa Yehova sudzachoka