We Believe JesusFé, Esperança e Nova Vida

Yesaya 21

Biblica® Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero · nianja

← Yesaya 20 Yesaya Yesaya 22 →

1Uthenga wonena za chipululu cha mʼmbali mwa Nyanja.

2Ine ndaona zinthu zoopsa mʼmasomphenya:

3Chifukwa cha zimenezi thupi langa likunjenjemera ndi mantha,

4Mtima wanga ukugunda,

5Ankhondo a ku Elamu ndi Mediya akukonza matebulo,

6Zimene Ambuye akunena kwa ine ndi izi;

7Taonani, anthu akubwera ali pa akavalo

8Ndipo mlondayo anafuwula kuti,

9Taonani, uyo munthu akubwera atakwera pa galeta

10Inu anthu anga opunthidwa ndi kupetedwa ngati tirigu,

11Uthenga wonena za Duma:

12Mlonda akuyankha kuti,

13Uthenga wonena za Arabiya:

14perekani madzi kwa anthu aludzu.

15Iwo akuthawa malupanga,

16Zimene Ambuye akunena kwa ine ndi izi: “Chaka chimodzi chisanathe, potsata mmene amawerengera munthu waganyu, ulemerero wonse wa Kedara udzatheratu.

17Mwa anthu okoka uta, ankhondo a ku Kedara opulumuka adzakhala owerengeka.” Wayankhula ndi Yehova Mulungu wa Israeli.

← Yesaya 20 Yesaya Yesaya 22 →