1Uzikumbukira mlengi wako
2Nthawi ya ukalamba wako, dzuwa ndi kuwala,
3Nthawi imene manja ako adzanjenjemera,
4Makutu ako adzatsekeka,
5Imeneyi ndiyo nthawi imene anthu amaopa kupita kumalo okwera,
6Kumbukira Iye chingwe cha siliva chisanaduke,
7Iyi ndi nthawi imene thupi lidzabwerera ku dothi, kumene linachokera,
8“Zopanda phindu! Zopandapake!” akutero Mlaliki.
9Mlaliki sanali wozindikira zinthu kokha ayi, komanso ankaphunzitsa anthu. Iye ankasinkhasinkha ndi kufufuzafufuza ndi kulemba mwadongosolo miyambi yambiri.
10Mlaliki anafufuzafufuza kuti apeze mawu oyenera, ndipo zimene analemba zinali zolondola ndiponso zoona.
11Mawu a anthu anzeru ali ngati zisonga, zokamba zawo zimene anasonkhanitsa zili ngati misomali yokhomera, yoperekedwa ndi mʼbusa mmodzi.
12Samalira mwana wanga, za kuwonjezera chilichonse pa zimenezi.
13Basi zonse zamveka; mathero a nkhaniyi ndi awa:
14Pakuti Mulungu adzaweruza zochita zonse,