We Believe JesusFé, Esperança e Nova Vida

Deuteronomo 32

Biblica® Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero · nianja

← Deuteronomo 31 Deuteronomo Deuteronomo 33 →

1Mverani, inu mayiko a mmwamba ndipo ine ndidzayankhula;

2Chiphunzitso changa chigwe ngati mvula

3Ndidzalalikira dzina la Yehova.

4Iye ndi Thanthwe, ntchito zake ndi zangwiro,

5Koma iwo achita mosakhulupirika pamaso pake,

6Kodi mukumubwezera Yehova chotere,

7Kumbukirani masiku amakedzana;

8Pamene Wammwambamwamba anapereka mayiko kwa anthu a mitundu ina kukhala cholowa chawo,

9Pakuti gawo la Yehova ndi anthu ake,

10Anamupeza mʼchipululu,

11ngati chiwombankhanga chimene chimasasula chisa chake

12Yehova yekha ndiye anamutsogolera;

13Anamuyendetsa pamwamba pa mapiri a mʼdziko

14pamodzi ndi chambiko ndi mkaka wochokera ku ngʼombe ndi nkhosa,

15Yesuruni ananenepa ndi kuyamba kuwukira;

16Anamuchititsa nsanje ndi milungu yawo yachilendo

17Anapereka nsembe kwa ziwanda zimene si Mulungu,

18Inu munasiya Thanthwe limene linakulerani;

19Yehova anaona zimenezi ndipo anawakana

20Iye anati, “Ndidzawabisira nkhope yanga,

21Anandichititsa kukhala wansanje pamene ankapembedza chimene si mulungu

22Pakuti mkwiyo wanga wayaka ngati moto,

23“Ndidzawawunjikira masautso

24Ndidzawatumizira njala yoopsa,

25Mʼmisewu lupanga lidzawasandutsa kukhala wopanda ana;

26Ine ndinanena kuti ndidzawamwaza

27koma sindinafune kuti adani anga adzandinyoze,

28Iwo ndi mtundu wopanda maganizo,

29Ngati iwo akanakhala anzeru akanamvetsetsa izi

30Kodi munthu mmodzi akanathamangitsa bwanji anthu 1,000

31Pakuti thanthwe lawo silofanana ndi Thanthwe lathu,

32Mpesa wawo umachokera ku mpesa wa ku Sodomu

33Vinyo wawo ndi wa ululu wa njoka,

34“Kodi zimenezi sindinazisunge

35Kubwezera chilango nʼkwanga; ndidzawalanga ndine.

36Yehova adzaweruza anthu ake

37Iye adzanena kuti, “Nanga ili kuti milungu yawo,

38milungu imene inkadya mafuta a nsembe zawo

39“Onani tsopano kuti Ine ndine Iyeyo!

40Ndikweza dzanja langa kumwamba ndi kulumbira kuti,

41pamene ndidzanola lupanga langa lonyezimira

42Mivi yanga idzakhuta magazi awo

43Kondwerani, inu mitundu yonse ya anthu pamodzi ndi anthu ake,

44Mose anabwera ndi Yoswa mwana wa Nuni ndipo anayankhula mawu onsewa mʼnyimbo anthu akumva.

45Mose atatsiriza kunena mawu onsewa pamtima kwa Aisraeli,

46iye anawawuza kuti, “Muwasunge bwino mu mtima mwanu, mawu onse amene lero lino ndikukuwuzani kuti mudzawuze ana anu, kuti adzamvere mosamalitsa mawu onse a malamulo amenewa.

47Mawuwa sikuti ndi mawu achabe kwa inu. Mawuwa ndi moyo wanu. Mukawamvera mudzakhala ndi moyo wautali mʼdziko limene mukukalitenga kukhala lanu mukawoloka Yorodani.”

48Tsiku lomwelo Yehova anawuza Mose kuti,

49“Pita ku mapiri a ku Abarimu ukakwere pa Phiri la Nebo ku Mowabu, moyangʼanana ndi Yeriko, ndipo ukaone dziko la Kanaani, dziko limene ndikulipereka kwa Aisraeli kukhala lawo.

50Iwe udzafera pa phiri limenelo ndipo udzapita kumene makolo ako anapita, monga mʼbale wako Aaroni anafera pa phiri la Hori ndipo anakakhala ndi anthu a mtundu wake.

51Chifukwa chake nʼchakuti inu nonse awiri simunakhulupirike kwa Ine pamaso pa Aisraeli pa madzi a Meriba ku Kadesi mʼchipululu cha Zini chifukwa simunandilemekeze kokwanira pakati pa Aisraeli.

52Choncho udzalionera kutali dziko limene ndikupereka kwa Aisraeli. Sudzalowa mʼdziko limene ndi kulipereka kwa Aisraeli.”

← Deuteronomo 31 Deuteronomo Deuteronomo 33 →