1Zimene Ambuye Yehova anandionetsa ndi izi: dengu la zipatso zakupsa.
2Iye anandifunsa kuti, “Amosi nʼchiyani ukuona?”
3“Tsiku limenelo,” Ambuye Yehova akulengeza kuti, “Nyimbo za mʼNyumba ya Mulungu zidzasanduka kulira kofuwula. Mitembo ya anthu idzachuluka, ndipo adzayiponya ponseponse! Kudzangoti zii!”
4Imvani izi, inu amene mumapondereza anthu osowa
5Mumanena kuti,
6tigule osauka ndi ndalama zasiliva
7Yehova amene Yakobo amamunyadira, walumbira kuti: Ine sindidzayiwala chilichonse chimene anachita.
8“Kodi dziko silidzagwedezeka chifukwa cha zimenezi,
9“Tsiku limenelo,” Ambuye Yehova akunena kuti,
10Maphwando anu achipembedzo ndidzawasandutsa kulira kwa chisoni
11“Nthawi ikubwera,” Ambuye Yehova akunena kuti,
12Anthu azidzangoyendayenda kuchoka ku nyanja ina kupita ku nyanja ina.
13“Tsiku limenelo
14Onse amene amalumbira pa tchimo la Samariya,