We Believe JesusFé, Esperança e Nova Vida

Amosi 6

Biblica® Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero · nianja

← Amosi 5 Amosi Amosi 7 →

1Tsoka kwa amene simukulabadira kanthu ku Ziyoni,

2Pitani ku mzinda wa Kaline mukawuyangʼane;

3Inu simulabadirako kuti tsiku loyipa lidzafika,

4Mumagona pa mabedi owakongoletsa ndi minyanga ya njovu,

5Mumayimba azeze anu ndi kumangopeka

6Mumamwera vinyo mʼzipanda zodzaza

7Nʼchifukwa chake inu mudzakhala mʼgulu la anthu oyamba kupita ku ukapolo;

8Ambuye Yehova walumbira mʼdzina lake. Yehova Mulungu Wamphamvuzonse walengeza kuti,

9Ngati anthu khumi otsala adzabisala mʼnyumba imodzi, nawonso adzafa ndithu.

10Ndipo ngati mʼbale wake wa wina wakufayo, woyenera kusamala za maliro, adzafika kudzatulutsa mitembo mʼnyumbamo nʼkufunsa aliyense amene akubisalabe mʼnyumbamo kuti, “Kodi uli ndi wina wamoyo mʼmenemo?” Ndipo munthu wobisalayo ndi kuyankha kuti, “Ayi,” mʼbaleyo adzanena kuti, “Khala chete! Ife tisayerekeze kutchula dzina la Yehova.”

11Pakuti Yehova walamula kuti

12Kodi akavalo amathamanga pa thanthwe?

13Inu amene mukunyadira kuti munagonjetsa Lo Debara

14Koma Yehova Mulungu Wamphamvuzonse akulengeza kuti,

← Amosi 5 Amosi Amosi 7 →