We Believe JesusFé, Esperança e Nova Vida

1 Mbiri 7

Biblica® Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero · nianja

← 1 Mbiri 6 1 Mbiri 1 Mbiri 8 →

1Ana a Isakara anali awa:

2Ana a Tola ndi awa:

3Mwana wa Uzi anali

4Monga mwa chiwerengero cha mabanja awo, panali anthu 36,000 odziwa kumenya nkhondo, pakuti iwo anali ndi akazi ndi ana ambiri.

5Abale awo onse a mʼbanja la Isakara amene anali odziwa kumenya nkhondo analipo 87,000, olembedwa potsata mibado yawo.

6Ana atatu a Benjamini anali awa:

7Ana a Bela anali awa:

8Ana a Bekeri anali awa:

9Pa mndandanda wa mʼbado wawo panali atsogoleri a mabanja ndi anthu 20,200 odziwa kumenya nkhondo.

10Mwana wa Yediaeli anali

11Ana onsewa a Yediaeli anali atsogoleri a mabanja. Analipo anthu 17,200 amene anali okonzeka kupita ku nkhondo.

12Asupi ndi Ahupi anali zidzukulu za Iri, ndipo Ahusimu anali zidzukulu za Aheri.

13Ana a Nafutali anali awa:

14Ana a Manase anali awa:

15Makiri anatenga mkazi wa banja la Ahupi ndi Asupi. Mlongo wake anali Maaka.

16Maaka mkazi wa Makiri anabereka mwana wamwamuna ndipo anamutcha Perezi. Mʼbale wake anamutcha Seresi, ndipo ana ake anali Ulamu ndi Rakemu.

17Mwana wa Ulamu anali

18Mlongo wake Hamoleketi anabereka Isihodi, Abiezeri ndi Mahila.

19Ana a Semida anali:

20Ana a Efereimu anali awa:

21Zabadi,

22Efereimu, abambo awo, anawalira masiku ambiri, ndipo abale ake anabwera kudzamutonthoza.

23Kenaka anagona ndi mkazi wake, ndipo anakhala woyembekezera nabala mwana wamwamuna. Anamutcha dzina lake Beriya, chifukwa tsoka linagwera banja lake.

24Mwana wake wamkazi anali Seera, amene anamanga mzinda wa Beti-Horoni Wakumunsi, Wakumtunda kudzanso Uzeni-Seera.

25Mwana wina wa Efereimu anali Refa amene zidzukulu zake zinali Resefu,

26Ladani, Amihudi,

27Nuni

28Malo amene ankakhala anali Beteli ndi midzi yozungulira, cha kummawa kunali Naarani, Gezeri ndi midzi yake ya kumadzulo ndi Sekemu ndi midzi yake mpaka ku Aya ndi midzi yake.

29Mʼmbali mwa malire a Manase munali Beti-Seani, Taanaki, Megido ndi Dori, pamodzi ndi midzi yake. Zidzukulu za Yosefe mwana wa Israeli zimakhala mʼmizinda imeneyi.

30Ana a Aseri anali awa:

31Ana a Beriya anali awa:

32Heberi anabereka Yafuleti, Someri, Hotamu ndi Suwa, mlongo wawo.

33Ana a Yafuleti anali awa:

34Ana a Someri anali awa:

35Ana a mʼbale wake Helemu anali awa:

36Ana a Zofa anali awa:

37Bezeri, Hodi, Sama, Silisa, Itirani ndi Bera.

38Ana a Yeteri anali awa:

39Ana a Ula anali awa:

40Onsewa anali zidzukulu za Aseri, atsogoleri a mabanja, anthu omveka, ankhondo olimba mtima, ndi akuluakulu pakati pa atsogoleri anzawo. Chiwerengero cha anthu odziwa kumenya nkhondo chomwe chinalembedwa chinali 26,000.

← 1 Mbiri 6 1 Mbiri 1 Mbiri 8 →