We Believe JesusFé, Esperança e Nova Vida

1 Mbiri 25

Biblica® Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero · nianja

← 1 Mbiri 24 1 Mbiri 1 Mbiri 26 →

1Davide ndi atsogoleri a asilikali anapatula ena mwa ana a Asafu, Hemani ndi Yedutuni ku utumiki wa uneneri pogwiritsa ntchito apangwe, azeze ndi ziwaya zamalipenga. Tsopano nawu mndandanda wa anthu amene ankagwira ntchito imeneyi:

2Kuchokera kwa ana a Asafu:

3Kwa Yedutuni, kuchokera kwa ana ake:

4Kwa Hemani, kuchokera kwa ana ake:

5Onsewa anali ana a Hemani mlosi wa mfumu. Iye anapatsidwa anawa potsata mawu a Mulungu akuti adzamukweza. Mulungu anapatsa Hemani ana aamuna 14 ndi ana aakazi atatu.

6Anthu onsewa ankayangʼaniridwa ndi makolo awo pa mayimbidwe a mʼNyumba ya Yehova. Iwowatu ankayimba ndi ziwaya zamalipenga, azeze ndi apangwe potumikira mʼNyumba ya Mulungu. Koma Asafu, Yedutuni ndi Hemani amayangʼaniridwa ndi mfumu.

7Iwo pamodzi ndi abale awo onse ophunzitsidwa ndi aluso loyimbira Yehova chiwerengero chawo chinali 288.

8Angʼonoangʼono ndi akulu omwe, mphunzitsi ndi wophunzira yemwe anachita maere pa ntchito zawo.

9Maere woyamba amene anali a Asafu, anagwera Yosefe,

10Maere achitatu anagwera Zakuri,

11Maere achinayi anagwera Iziri,

12Maere achisanu anagwera Netaniya,

13Maere achisanu ndi chimodzi anagwera Bukiya,

14Maere achisanu ndi chiwiri anagwera Yesarela,

15Maere achisanu ndi chitatu anagwera Yeshaya,

16Maere achisanu ndi chinayi anagwera Mataniya,

17Maere a khumi anagwera Simei,

18Maere a 11 anagwera Azareli,

19Maere a 12 anagwera Hasabiya,

20Maere a 13 anagwera Subaeli,

21Maere a 14 anagwera Matitiya,

22Maere a 15 anagwera Yeremoti,

23Maere a 16 anagwera Hananiya,

24Maere a 17 anagwera Yosibakasa,

25Maere a 18 anagwera Hanani,

26Maere a 19 anagwera Maloti,

27Maere a 20 anagwera Eliyata,

28Maere a 21 anagwera Hotiri,

29Maere a 22 anagwera Gidaliti,

30Maere a 23 anagwera Mahazioti,

31Maere a 24 anagwera Romamiti-Ezeri,

← 1 Mbiri 24 1 Mbiri 1 Mbiri 26 →