We Believe JesusFé, Esperança e Nova Vida

Yeremiya 20

Biblica® Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero · nianja

← Yeremiya 19 Yeremiya Yeremiya 21 →

1Wansembe Pasuri mwana wa Imeri, woyangʼanira wamkulu wa Nyumba ya Yehova, anamva Yeremiya akulosera zinthu zimenezi.

2Tsono iye analamula kuti mneneri Yeremiyayo amenyedwe ndi kuyikidwa mʼndende pa Chipata chakumtunda kwa Benjamini ku Nyumba ya Yehova.

3Mmawa mwake, Pasuri anatulutsa Yeremiya mʼndende, ndipo Yeremiyayo anamuwuza kuti, “Pasuri, Yehova sadzakutchulanso dzina lako kuti Pasuri koma Zoopsa pa Mbali Zonse.

4Pakuti Yehova akuti, ‘Ndidzakusandutsa choopsa kwa mwiniwakewe ndi kwa abwenzi ako onse; iweyo ukuona. Anthu a ku Yuda ndidzawapereka onse mʼmanja mwa mfumu ya ku Babuloni. Ena adzatengedwa ukapolo ku Babuloni ndipo ena adzaphedwa pa nkhondo.

5Ndidzapereka kwa adani awo chuma chonse cha mu mzinda uno, phindu lonse la ntchito yake, zinthu zake zonse za mtengowapatali ndiponso katundu yense wa mafumu a ku Yuda. Iwo adzazitenga monga zinthu zolanda ku nkhondo ndi kupita nazo ku Babuloni.

6Ndipo iwe, Pasuri, pamodzi ndi onse a pa banja pako mudzapita ku ukapolo ku Babuloni. Mudzafera kumeneko ndi kuyikidwa mʼmanda, iweyo pamodzi ndi abwenzi ako amene unawalosera zabodza.’ ”

7Inu Yehova, mwandinamiza, ndipo ndinapusadi;

8Nthawi iliyonse ndikamayankhula,

9Koma ndikanena kuti, “Sindidzalalikiranso za Iye

10Ndimamva anthu ambiri akunongʼona kuti,

11Koma Yehova ali nane, ndiye wankhondo wamphamvu.

12Inu Yehova Wamphamvuzonse, Inu amene mumayesa anthu molungama

13Imbirani Yehova!

14Litembereredwe tsiku limene ndinabadwa!

15Wotembereredwa munthu amene anapita kukasangalatsa abambo anga

16Munthu ameneyo akhale ngati mizinda imene

17Chifukwa sanandiphere mʼmimba,

18Kodi ndinabadwira mavuto ndi chisoni

← Yeremiya 19 Yeremiya Yeremiya 21 →