1Pambuyo pake Yakobo anayitanitsa ana ake aamuna nati: Sonkhanani pamodzi kuti ndikuwuzeni zimene zidzakuchitikireni mʼmasiku a mʼtsogolo.
2“Bwerani ndipo imvani mawu anga, inu ana a Yakobo;
3“Rubeni, ndiwe woyamba kubadwa;
4Wokokoma ngati madzi a chigumula, koma sudzakhalanso wopambana,
5“Simeoni ndi Levi ndi pachibale pawo,
6Iwe moyo wanga, usakhale nawo pa misonkhano yawo ya mseri,
7Matemberero awagwere chifukwa cha mkwiyo wawo woopsa chonchi
8“Yuda, ndiwe amene abale ako adzatamanda;
9Yuda ali ngati mwana wa mkango;
10Ndodo yaufumu sidzachoka mwa Yuda,
11Ndiye amene amamangirira bulu wake wamkazi kumtengo wa mpesa,
12Maso ake adzakhala akuda chifukwa cha vinyo,
13“Zebuloni adzakhala mʼmphepete mwa nyanja;
14“Isakara ali ngati bulu wamphamvu
15Ataona ubwino wake wa pamalo pake popumira
16“Dani adzaweruza mwachilungamo anthu ake
17Dani adzakhala ngati njoka ya mʼmphepete mwa msewu,
18“Ndikuyembekeza chipulumutso chanu Yehova.
19“Gadi adzachitidwa chiwembu ndi gulu la amaliwongo,
20“Dziko la Aseri lidzabereka chakudya chokoma,
21“Nafutali ali ngati mbawala yayikazi
22“Yosefe ali ngati mtengo wobereka zipatso,
23Alenje a uta anamuchita chiwembu mwankhanza;
24Koma uta wake sunagwedezeke,
25Chifukwa cha Mulungu wa makolo ako amene amakuthandiza;
26Madalitso a kholo lako ndi amphamvu kuposa
27“Benjamini ali ngati mʼmbulu wolusa;
28Onse awa ndi mafuko khumi ndi awiri a Israeli, ndipo zimenezi ndi zomwe abambo awo ananena pamene anawadalitsa, kuwapatsa aliyense madalitso ake womuyenera iye.
29Kenaka Yakobo analamula ana ake nati: “Ine ndatsala pangʼono kufa. Tsono mukandiyike pamodzi ndi makolo anga mʼphanga la mʼmunda wa Efroni Mhiti.
30Ili ndi phanga la mʼmunda wa Makipela, pafupi ndi Mamre mʼdziko la Kanaani. Abrahamu anagula phangalo pamodzi ndi munda womwe kwa Efroni Mhiti kuti pakhale manda.
31Kumeneko kunayikidwa Abrahamu ndi mkazi wake Sara, Isake ndi mkazi wake Rebeka ndipo ndinayikakonso Leya.
32Munda ndi manda amene ali mʼmenemo zinagulidwa kwa Ahiti.”
33Yakobo atamaliza kupereka malangizo kwa ana ake, anabwezera miyendo yake pa bedi, namwalira ndipo anakakhala ndi anthu a mtundu wake.